Ricky Wang

Ndine wophunzira wa udokotala ku New York City. Ndimaganiza kuti umoyo ndi ufulu wa chibadwidwe. Ndinagwira ntchito miyezi naini ku Malawi. Ndinapatsa ana onyentchera ndi otupikana chiponde.

I'm a medical student at Weill Medical College of Cornell University. I'm an advocate for global health equity. I've worked for 9 months as a field clinician in Malawi treating children with acute malnutrition.